x

You are using an outdated browser. Please upgrade your browser to improve your ReverbNation experience.

LETSON KAMPHONJE / Blog

TIRIKUZIWA

FIRST VERSE:1

Mwanthawi zonse kupanga choyipa chimakoma ndiponso chimamaphweka. Koma vuto ubale ndimulungu timawusokoneza mchifukwa tizikhala ochenjera kuti tipewe misampha ya satana,chifukwa akulu amenewa akuyendayendapadzikopano kufunafuna omuwononga

Feedback